Loading...

Download
  • Genre:Hip Hop & Rap
  • Year of Release:2023

Lyrics

Eh

Kuona maso a khono nkudekha

Zabwino

Zabwino eh

Zili mtsogolo


Let's go


Chibwana chimalanga ukapanda kuchenjela

Azinzako umacheza nao akulemela

Iwe kumangomwa mowa kumazilekelela

Tsegula maso ako zabwino zili


Mtsogolo

Mtsogolo

Mtsogolo

Mtsogolo

Zabwino zili

Mtsogolo

Mtsogolo

Mtsogolo

Mtsogolo

Zabwino zili


Zabwino mwati zilikuti?

Ndakhalila saka mwayi ulikuti?

Pena kuluza hope hope hope kodi ndilikuti?

Kudusa muzi kho khomo mmatope kumwela codeine

Kumazifusa ndinabwelelanji kuzindikila sizingangochitika

Nanga ndikumalakwisa pati chilipo chomwe sichikumachitika

Sukusuntha sintha company

Simakhalisa iwe life yapano

Zabwino zili mtsogolo nzasangalala

Pano nduphaka nzelu kenako nzaphaka ka life

Kungopeza change ndeno nzapeza ka wife mmh

Chibwana chimalanda life


Chibwana chimalanga ukapanda kuchenjela

Azizako umacheza nao akulemela

Iwe kumangomwa mowa kumazilekelela

Tsegula maso ako zabwino zili


Mtsogolo

Mtsogolo

Mtsogolo

Mtsogolo

Zabwino zili

Mtsogolo

Mtsogolo

Mtsogolo

Mtsogolo

Zabwino zili


Yeah yeyeye yeah

Zabwino zili mtsogolo

Yeah ey ey maso pa ey

Maso pa tsogolo

Similar Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status